-
Yeremiya 11:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Makolo anu ndinawalamula kuti azimvera mawu amenewa pamene ndinkawatulutsa mʼdziko la Iguputo,+ pamene ndinkawatulutsa mʼngʼanjo yosungunulira zitsulo.+ Ndinawalamula kuti, ‘Muzimvera mawu anga, ndipo muzichita zinthu zonse zimene ndakulamulani. Mukatero mudzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu,+
-