Yeremiya 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 kuti ndikwaniritse lumbiro limene ndinalumbirira makolo anu kuti ndidzawapatsa dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ ngati mmene zilili lero.’”’” Pamenepo ine ndinayankha kuti: “Zikhale momwemo,* inu Yehova.”
5 kuti ndikwaniritse lumbiro limene ndinalumbirira makolo anu kuti ndidzawapatsa dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ ngati mmene zilili lero.’”’” Pamenepo ine ndinayankha kuti: “Zikhale momwemo,* inu Yehova.”