Yeremiya 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inetu ndinkalangiza makolo anu pa tsiku limene ndinawatulutsa mʼdziko la Iguputo ndipo ndikupitiriza mpaka pano. Ndinkawalangiza mobwerezabwereza* kuti: “Muzimvera mawu anga.”+
7 Inetu ndinkalangiza makolo anu pa tsiku limene ndinawatulutsa mʼdziko la Iguputo ndipo ndikupitiriza mpaka pano. Ndinkawalangiza mobwerezabwereza* kuti: “Muzimvera mawu anga.”+