Yeremiya 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo abwerera ku zolakwa za makolo awo akale amene anakana kumvera mawu anga.+ Iwonso atsatira milungu ina ndipo akuitumikira.+ A mʼnyumba ya Isiraeli ndi a mʼnyumba ya Yuda aphwanya pangano langa limene ndinachita ndi makolo awo.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:10 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 9
10 Iwo abwerera ku zolakwa za makolo awo akale amene anakana kumvera mawu anga.+ Iwonso atsatira milungu ina ndipo akuitumikira.+ A mʼnyumba ya Isiraeli ndi a mʼnyumba ya Yuda aphwanya pangano langa limene ndinachita ndi makolo awo.+