Yeremiya 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Yehova wanena kuti, ‘Ndiwagwetsera tsoka+ limene sadzatha kulithawa. Akadzandiitana kuti ndiwathandize, sindidzawamvetsera.+
11 Choncho Yehova wanena kuti, ‘Ndiwagwetsera tsoka+ limene sadzatha kulithawa. Akadzandiitana kuti ndiwathandize, sindidzawamvetsera.+