Yeremiya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno mizinda ya Yuda komanso anthu okhala mu Yerusalemu adzapita kukapempha thandizo kwa milungu imene akuifukizira nsembe.+ Koma milungu imeneyo sidzawapulumutsa pa nthawi ya tsoka lawo.
12 Ndiyeno mizinda ya Yuda komanso anthu okhala mu Yerusalemu adzapita kukapempha thandizo kwa milungu imene akuifukizira nsembe.+ Koma milungu imeneyo sidzawapulumutsa pa nthawi ya tsoka lawo.