Yeremiya 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa milungu yako, iwe Yuda, yafanana ndi mizinda yako kuchuluka kwake. Ndipo chinthu chochititsa manyazi mwachimangira* maguwa ansembe ochuluka mofanana ndi misewu ya mu Yerusalemu, maguwa ansembe oti muziperekerapo nsembe kwa Baala.’+
13 Chifukwa milungu yako, iwe Yuda, yafanana ndi mizinda yako kuchuluka kwake. Ndipo chinthu chochititsa manyazi mwachimangira* maguwa ansembe ochuluka mofanana ndi misewu ya mu Yerusalemu, maguwa ansembe oti muziperekerapo nsembe kwa Baala.’+