Yeremiya 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yehova wa magulu ankhondo akumwamba amaweruza mwachilungamo.Amafufuza maganizo* komanso mtima.+ Inu Mulungu, ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango,Chifukwa mlandu wanga ndausiya mʼmanja mwanu.
20 Koma Yehova wa magulu ankhondo akumwamba amaweruza mwachilungamo.Amafufuza maganizo* komanso mtima.+ Inu Mulungu, ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango,Chifukwa mlandu wanga ndausiya mʼmanja mwanu.