Yeremiya 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho izi ndi zimene Yehova wanena zokhudza anthu a ku Anatoti+ amene akufuna kuchotsa moyo wako, ndipo akunena kuti: “Usanenere mʼdzina la Yehova+ ngati ukufuna kuti tisakuphe.”
21 Choncho izi ndi zimene Yehova wanena zokhudza anthu a ku Anatoti+ amene akufuna kuchotsa moyo wako, ndipo akunena kuti: “Usanenere mʼdzina la Yehova+ ngati ukufuna kuti tisakuphe.”