Yeremiya 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Ine ndidzawapatsa chilango. Anyamata adzafa ndi lupanga+ ndipo ana awo aamuna ndi aakazi adzafa ndi njala.+
22 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Ine ndidzawapatsa chilango. Anyamata adzafa ndi lupanga+ ndipo ana awo aamuna ndi aakazi adzafa ndi njala.+