Yeremiya 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Cholowa changa chili ngati mbalame yanthenga zamitundu yosiyanasiyana imene imadya nyama.Mbalame zina zodya nyama zaizungulira nʼkuiukira.+ Bwerani, sonkhanani pamodzi inu nyama zonse zamʼtchire,Bwerani kuti mudzadye.+
9 Cholowa changa chili ngati mbalame yanthenga zamitundu yosiyanasiyana imene imadya nyama.Mbalame zina zodya nyama zaizungulira nʼkuiukira.+ Bwerani, sonkhanani pamodzi inu nyama zonse zamʼtchire,Bwerani kuti mudzadye.+