Yeremiya 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu owononga adutsa mʼnjira zonse zodutsidwadutsidwa zamʼchipululu,Chifukwa lupanga la Yehova likuwononga anthu kuchokera kumalekezero a dziko kukafika kumalekezero ena a dziko.+ Ndipo palibe munthu aliyense amene ali pamtendere.
12 Anthu owononga adutsa mʼnjira zonse zodutsidwadutsidwa zamʼchipululu,Chifukwa lupanga la Yehova likuwononga anthu kuchokera kumalekezero a dziko kukafika kumalekezero ena a dziko.+ Ndipo palibe munthu aliyense amene ali pamtendere.