-
Yeremiya 12:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Koma ndikadzawazula, ndidzawachitiranso chifundo moti ndidzabwezeretsa aliyense wa iwo pacholowa chake ndi pamalo ake.
-