-
Yeremiya 12:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndiyeno anthu a mitundu ina akadzayesetsa kuphunzira njira za anthu anga ndi kulumbira mʼdzina langa kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo!’ ngati mmene iwo anaphunzitsira anthu anga kulumbira mʼdzina la Baala, anthu a mitundu inawo adzakhazikika pakati pa anthu anga.
-