Yeremiya 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu oipawa, amene akukana kumvera mawu anga,+ amene mouma khosi amatsatira zofuna za mitima yawo+ ndipo akutsatira milungu ina, akuitumikira komanso kuigwadira, adzakhala ngati lamba ameneyu amene sangagwirenso ntchito iliyonse.’
10 Anthu oipawa, amene akukana kumvera mawu anga,+ amene mouma khosi amatsatira zofuna za mitima yawo+ ndipo akutsatira milungu ina, akuitumikira komanso kuigwadira, adzakhala ngati lamba ameneyu amene sangagwirenso ntchito iliyonse.’