Yeremiya 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako ukawauze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Inetu ndikuledzeretsa anthu onse amʼdzikoli,+ mafumu amene akukhala pampando wachifumu wa Davide, ansembe, aneneri ndi anthu onse amene amakhala mu Yerusalemu.
13 Kenako ukawauze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Inetu ndikuledzeretsa anthu onse amʼdzikoli,+ mafumu amene akukhala pampando wachifumu wa Davide, ansembe, aneneri ndi anthu onse amene amakhala mu Yerusalemu.