Yeremiya 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo ndidzawombanitsa munthu ndi mnzake, abambo chimodzimodzinso ana,” akutero Yehova.+ “Sindidzawakomera mtima, kuwamvera chisoni kapena kuwachitira chifundo. Palibe chimene chidzandilepheretse kuti ndiwawononge.”’+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:14 Yandikirani, tsa. 258
14 Ndipo ndidzawombanitsa munthu ndi mnzake, abambo chimodzimodzinso ana,” akutero Yehova.+ “Sindidzawakomera mtima, kuwamvera chisoni kapena kuwachitira chifundo. Palibe chimene chidzandilepheretse kuti ndiwawononge.”’+