Yeremiya 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mizinda yakumʼmwera yatsekedwa* ndipo palibe amene angaitsegule. Anthu onse a mu Yuda atengedwa kupita ku ukapolo. Onse atengedwa kupita ku ukapolo popanda wotsala.+
19 Mizinda yakumʼmwera yatsekedwa* ndipo palibe amene angaitsegule. Anthu onse a mu Yuda atengedwa kupita ku ukapolo. Onse atengedwa kupita ku ukapolo popanda wotsala.+