Yeremiya 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo ukadzanena mumtima mwako kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani zinthu zimenezi zandigwera?’+ Udzadziwe kuti wavulidwa siketi yako chifukwa cha kuchuluka kwa machimo ako+ Ndipo zidendene zako zazunzidwa.
22 Ndipo ukadzanena mumtima mwako kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani zinthu zimenezi zandigwera?’+ Udzadziwe kuti wavulidwa siketi yako chifukwa cha kuchuluka kwa machimo ako+ Ndipo zidendene zako zazunzidwa.