Yeremiya 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho ndidzakuvula siketi yako nʼkukuphimba nayo kumaso,Ndipo anthu adzaona maliseche ako.+