Yeremiya 13:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chigololo chimene ukuchita,+ kumemesa* kwako,Khalidwe lako lonyansa* la uhule, zonsezi zidzaonekera. Ndaona khalidwe lako lonyansa+Mʼmapiri komanso kuthengo. Tsoka kwa iwe Yerusalemu! Kodi ukhalabe wodetsedwa mpaka liti?”+
27 Chigololo chimene ukuchita,+ kumemesa* kwako,Khalidwe lako lonyansa* la uhule, zonsezi zidzaonekera. Ndaona khalidwe lako lonyansa+Mʼmapiri komanso kuthengo. Tsoka kwa iwe Yerusalemu! Kodi ukhalabe wodetsedwa mpaka liti?”+