Yeremiya 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yuda akulira maliro+ ndipo mageti ake agwa. Agwa pansi nʼkumalira momvetsa chisoni,Ndipo anthu a ku Yerusalemu akulira.
2 Yuda akulira maliro+ ndipo mageti ake agwa. Agwa pansi nʼkumalira momvetsa chisoni,Ndipo anthu a ku Yerusalemu akulira.