-
Yeremiya 14:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Anthu awo olemekezeka amatuma antchito awo kuti akatunge madzi.
Antchitowo amapita kuzitsime koma sapezako madzi.
Amabwerako ndi ziwiya zopanda kanthu.
Iwo achita manyazi ndipo akhumudwa,
Moti aphimba mitu yawo.
-