Yeremiya 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abulu amʼtchire angoima mʼmapiri opanda kanthu. Akupuma mwawefuwefu ngati mimbulu.Maso awo achita mdima chifukwa kulibe msipu.+
6 Abulu amʼtchire angoima mʼmapiri opanda kanthu. Akupuma mwawefuwefu ngati mimbulu.Maso awo achita mdima chifukwa kulibe msipu.+