Yeremiya 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale kuti machimo athu akuchitira umboni kuti ndife olakwa,Inu Yehova, chitanipo kanthu chifukwa cha dzina lanu.+ Chifukwa zochita zathu zosonyeza kusakhulupirika nʼzambiri,+Ndipo takuchimwirani.
7 Ngakhale kuti machimo athu akuchitira umboni kuti ndife olakwa,Inu Yehova, chitanipo kanthu chifukwa cha dzina lanu.+ Chifukwa zochita zathu zosonyeza kusakhulupirika nʼzambiri,+Ndipo takuchimwirani.