Yeremiya 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu chiyembekezo cha Isiraeli, Mpulumutsi wake+ pa nthawi yamavuto,Nʼchifukwa chiyani mukukhala ngati mlendo mʼdzikoli?Nʼchifukwa chiyani mukukhala ngati munthu wapaulendo amene waima kuti agone usiku umodzi wokha? Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:8 Galamukani!,5/8/2004, tsa. 19
8 Inu chiyembekezo cha Isiraeli, Mpulumutsi wake+ pa nthawi yamavuto,Nʼchifukwa chiyani mukukhala ngati mlendo mʼdzikoli?Nʼchifukwa chiyani mukukhala ngati munthu wapaulendo amene waima kuti agone usiku umodzi wokha?