Yeremiya 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Akamasala kudya, ine sindimvetsera kuchonderera kwawo.+ Akamapereka nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zambewu, ine sindisangalala nazo+ ndipo ndiwawononga ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.”*+
12 Akamasala kudya, ine sindimvetsera kuchonderera kwawo.+ Akamapereka nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zambewu, ine sindisangalala nazo+ ndipo ndiwawononga ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.”*+