Yeremiya 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu Yehova, ife tikuvomereza zinthu zoipa zimene tachitaKomanso kulakwa kwa makolo athu,Chifukwa takuchimwirani.+
20 Inu Yehova, ife tikuvomereza zinthu zoipa zimene tachitaKomanso kulakwa kwa makolo athu,Chifukwa takuchimwirani.+