Yeremiya 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma chifukwa cha dzina lanu, musatikane.+Musachititse manyazi mpando wanu wachifumu waulemerero. Kumbukirani pangano limene munachita ndi ife ndipo musaliphwanye.+
21 Koma chifukwa cha dzina lanu, musatikane.+Musachititse manyazi mpando wanu wachifumu waulemerero. Kumbukirani pangano limene munachita ndi ife ndipo musaliphwanye.+