Yeremiya 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Yehova anandiuza kuti: “Ngakhale Mose ndi Samueli akanaima pamaso panga,+ anthu awa sindikanawakomera mtima. Achotse pamaso panga. Asiye apite.
15 Kenako Yehova anandiuza kuti: “Ngakhale Mose ndi Samueli akanaima pamaso panga,+ anthu awa sindikanawakomera mtima. Achotse pamaso panga. Asiye apite.