Yeremiya 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ndidzawabweretsera masoka okwanira 4,’*+ akutero Yehova. ‘Ndidzawatumizira lupanga kuti liwaphe, agalu kuti akoke mitembo yawo, mbalame zamumlengalenga komanso zilombo zakutchire kuti ziwadye ndi kuwawononga.+
3 “‘Ndidzawabweretsera masoka okwanira 4,’*+ akutero Yehova. ‘Ndidzawatumizira lupanga kuti liwaphe, agalu kuti akoke mitembo yawo, mbalame zamumlengalenga komanso zilombo zakutchire kuti ziwadye ndi kuwawononga.+