-
Yeremiya 15:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndi ndani adzakusonyeze chifundo, iwe Yerusalemu?
Ndi ndani adzakumvere chisoni,
Ndipo ndi ndani adzapatuke kuti afunse za moyo wako?’
-