Yeremiya 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Iwe wandisiya,’ akutero Yehova.+ ‘Ukupitiriza kubwerera nʼkundisiya.*+ Choncho ndidzakutambasulira dzanja langa nʼkukuwononga.+ Ndatopa ndi kukumvera chisoni.*
6 ‘Iwe wandisiya,’ akutero Yehova.+ ‘Ukupitiriza kubwerera nʼkundisiya.*+ Choncho ndidzakutambasulira dzanja langa nʼkukuwononga.+ Ndatopa ndi kukumvera chisoni.*