Yeremiya 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzawapeta kuti auluzike ndi mphepo pamageti amʼdzikoli. Ndidzawaphera ana awo.+ Ndidzawononga anthu anga,Chifukwa akukana kusiya kuyenda mʼnjira zawo.+
7 Ndidzawapeta kuti auluzike ndi mphepo pamageti amʼdzikoli. Ndidzawaphera ana awo.+ Ndidzawononga anthu anga,Chifukwa akukana kusiya kuyenda mʼnjira zawo.+