Yeremiya 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsoka ine, chifukwa inu mayi anga munabereka ine,+Munthu amene nthawi zonse ndimakangana ndi dziko lonse komanso kulimbana nalo. Sindinakongole kanthu kapena kukongoza wina aliyense,Koma anthu onse akunditemberera.
10 Tsoka ine, chifukwa inu mayi anga munabereka ine,+Munthu amene nthawi zonse ndimakangana ndi dziko lonse komanso kulimbana nalo. Sindinakongole kanthu kapena kukongoza wina aliyense,Koma anthu onse akunditemberera.