-
Yeremiya 15:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Yehova anandiuza kuti: “Ndithu ndidzakuchitira zinthu zabwino.
Ndithu ndidzakuthandiza pa nthawi ya tsoka,
Ndidzakuthandiza pa nthawi yamavuto.
-