Yeremiya 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova mukudziwa bwino mavuto anga.Ndikumbukireni ndi kundiyangʼana. Mundibwezerere anthu amene akundizunza.+ Musalole kuti ndiwonongeke chifukwa chakuti mukuwalezera mtima. Dziwani kuti ndikunyozedwa chifukwa cha inu.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:15 Yeremiya, ptsa. 117-118
15 Inu Yehova mukudziwa bwino mavuto anga.Ndikumbukireni ndi kundiyangʼana. Mundibwezerere anthu amene akundizunza.+ Musalole kuti ndiwonongeke chifukwa chakuti mukuwalezera mtima. Dziwani kuti ndikunyozedwa chifukwa cha inu.+