-
Yeremiya 15:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Nʼchifukwa chiyani ululu wanga sukutha ndiponso bala langa silikupola?
Balali silikumva mankhwala.
Kodi mukhala ngati chitsime chosathandiza
Chimene munthu sangachidalire?
-