-
Yeremiya 16:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Palibe amene adzapereke chakudya kwa anthu amene akulira maliro,
Kuti awatonthoze chifukwa cha maliro amene awagwera,
Komanso palibe amene adzawapatse kapu ya vinyo kuti awatonthoze
Kuti amwe chifukwa cha imfa ya bambo awo kapena mayi awo.
-