Yeremiya 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Mʼmasiku anu, ndidzathetsa phokoso lachikondwerero, phokoso lachisangalalo, mawu a mkwati ndi mawu a mkwatibwi mʼmalo ano, inuyo mukuona.’+
9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Mʼmasiku anu, ndidzathetsa phokoso lachikondwerero, phokoso lachisangalalo, mawu a mkwati ndi mawu a mkwatibwi mʼmalo ano, inuyo mukuona.’+