Yeremiya 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ukadzauza anthu awa mawu onsewa, iwo adzakufunsa kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani Yehova wanena kuti adzatigwetsera tsoka lalikulu limeneli? Kodi talakwa chiyani ndipo tamuchimwira chiyani Yehova Mulungu wathu?’+
10 Ukadzauza anthu awa mawu onsewa, iwo adzakufunsa kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani Yehova wanena kuti adzatigwetsera tsoka lalikulu limeneli? Kodi talakwa chiyani ndipo tamuchimwira chiyani Yehova Mulungu wathu?’+