Yeremiya 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma adzalumbira kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa Aisiraeli mʼdziko lakumpoto komanso kuchokera mʼmayiko onse kumene anawabalalitsira!” Ineyo ndidzawabwezera kudziko lawo limene ndinapatsa makolo awo.’+
15 Koma adzalumbira kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa Aisiraeli mʼdziko lakumpoto komanso kuchokera mʼmayiko onse kumene anawabalalitsira!” Ineyo ndidzawabwezera kudziko lawo limene ndinapatsa makolo awo.’+