Yeremiya 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choyamba ndidzawabwezera zolakwa zawo zonse ndi machimo awo onse,+Chifukwa aipitsa dziko langa ndi zifaniziro zopanda moyo za mafano* awo onyansaNdipo adzaza cholowa changa ndi zinthu zawo zonyansa.’”+
18 Choyamba ndidzawabwezera zolakwa zawo zonse ndi machimo awo onse,+Chifukwa aipitsa dziko langa ndi zifaniziro zopanda moyo za mafano* awo onyansaNdipo adzaza cholowa changa ndi zinthu zawo zonyansa.’”+