Yeremiya 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwa kufuna kwanu, mudzataya cholowa chimene ndinakupatsani.+ Ndipo ndidzakuchititsani kuti mutumikire adani anu mʼdziko limene simukulidziwa.+Chifukwa mwayatsa mkwiyo wanga ngati moto.*+ Moto wake udzayakabe mpaka kalekale.”
4 Mwa kufuna kwanu, mudzataya cholowa chimene ndinakupatsani.+ Ndipo ndidzakuchititsani kuti mutumikire adani anu mʼdziko limene simukulidziwa.+Chifukwa mwayatsa mkwiyo wanga ngati moto.*+ Moto wake udzayakabe mpaka kalekale.”