-
Yeremiya 17:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Iye adzakhala ngati mtengo umene uli pawokhawokha mʼchipululu.
Zabwino zikadzafika sadzatha kuziona,
Koma adzakhala mʼmalo ouma amʼchipululu,
Mʼdziko la nthaka yamchere, kumene sikungakhale munthu aliyense.
-