Yeremiya 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu amene amapeza chuma mwachinyengo,*+Ali ngati nkhwali imene imasonkhanitsa mazira amene sinaikire. Chuma chakecho chidzatha asanakwanitse hafu ya zaka za moyo wake,Ndipo pamapeto pake adzadziwika kuti ndi wopusa.”
11 Munthu amene amapeza chuma mwachinyengo,*+Ali ngati nkhwali imene imasonkhanitsa mazira amene sinaikire. Chuma chakecho chidzatha asanakwanitse hafu ya zaka za moyo wake,Ndipo pamapeto pake adzadziwika kuti ndi wopusa.”