Yeremiya 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mpando waulemerero wa Mulungu ndi wokwezeka kuyambira pa chiyambi,Ndipo ndi malo athu opatulika.+