-
Yeremiya 17:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndipo ukawauze kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova, inu mafumu a Yuda ndi anthu nonse amene mukukhala mu Yuda komanso inu nonse amene mukukhala mu Yerusalemu, amene mumalowera pamageti awa.
-