Yeremiya 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Nyamuka, upite kunyumba ya woumba mbiya+ ndipo ndikakuuza mawu anga kumeneko.”