Yeremiya 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Inu a nyumba ya Isiraeli, kodi sindingakuchiteni zofanana ndi zimene woumba mbiyayu anachita?’ akutero Yehova. ‘Tamverani! Mofanana ndi dongo limene lili mʼmanja mwa woumba mbiya, ndi mmene inunso mulili kwa ine, inu nyumba ya Isiraeli.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:6 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,4/2017, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,4/1/1999, tsa. 22
6 “‘Inu a nyumba ya Isiraeli, kodi sindingakuchiteni zofanana ndi zimene woumba mbiyayu anachita?’ akutero Yehova. ‘Tamverani! Mofanana ndi dongo limene lili mʼmanja mwa woumba mbiya, ndi mmene inunso mulili kwa ine, inu nyumba ya Isiraeli.+